Phyzix - Bossn Up (Prod By Mwanie)

  • 1
  • 9
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0

Stream and download 04. Phyzix - Bossn Up (Prod By Mwanie)

Text

*BOSS'N UP by Phyzix*
Produced by Mwanie
FIGARO 7 (2024)

*INTRO*
Yeah
Mwanie

*VERSE 1*
Eh/ koma ndikudya zi money/ adokotala akuti ndisamazimane/ aseee pali zi mowa za mame/ moyo umakoma boys tisamadane/ (cheers) tizikondana tizitengana lende nkukankhana/ (cheers) tonse ndi anthu sitilephera pena kukangana/ zinthu zimatha pepani bwana si za kuthana kuthana/ zomasunga mpeni ku mphasa nza satana

*HOOK*
I'm boss'n up/ there's no limit/ ndikupanga zi Ndalama every minute
Oh/ I'm boss'n up/ Premier bet/ akumazipanga okha marinate
Bro/ I'm boss'n up/ sinsankha date/ tsiku lililonse kukweza geji
Bro/ I'm boss'n up/ Premier bet/ akumazipanga okha marinate/ Bro/ I'm boss'n up/

*VERSE 2*
Chase the money bro/ you can never lose the women/ amakhala ngati atumidwa to take you outta heaven/ wekha mpaka seven uzitoleretu bredrin/ hustle imafunika energy stop losing SEMEN/ usamakonde zokoka like you one of the SEA MEN/ amati akapita out they wanna SEE MEN/ panga zibwana nawe uzathe ngati phone ya SIEMENS/ chilungamo chake ndichokuti kuliri SI M’MENE/ Kumangokhala osahasa me?/ how can I?/ ndine wakale zedi kuli ma label a Karl Kani/ zaka zaka kumangopita khalidwe ngodya zinayi/ ndimakhala ngati mphaka nanenso moyo wanga ndi ka nine/

*HOOK*
I'm boss'n up/ there's no limit/ ndikupanga zi Ndalama every minute
Oh / I'm boss'n up/ Premier bet/ akumazipanga okha marinate
Bro/ I'm boss'n up/ sinsankha date/ tsiku lililonse kukweza geji
Bro/ I'm boss'n up/ Premier bet/ akumazipanga okha marinate/ Bro/ I'm boss'n up/

*VERSE 3*
Mafana akufuna andisizee/// (eh) muwauze ndilibe size eti/ kumati kukacha mpaka sunset/ daily hustle ngati daily ndi mwezi wa rent/ tsiku la ndalama sitisintha date/ olo utachoka undipeza ndili pa gate/ ndiku NDIKU ndiku NDIKU ndikudikilira/ zanga uzibweza ine sindisekelera/ pamakhala kuti pa malo patelera/ umazimva mlamba iweyo kutelera/ you can never lose women chasing the money bro/ amachita kumudziwa wa ndalamayo/

*HOOK*
I'm boss'n up/ there's no limit/ ndikupanga zi Ndalama every minute
Oh / I'm boss'n up/ Premier bet/ akumazipanga okha marinate
Bro/ I'm boss'n up/ sinsankha date/ tsiku lililonse kukweza geji
Bro/ I'm boss'n up/ Premier bet/ akumazipanga okha marinate/ Bro/ I'm boss'n up/

It’s Only Entertainment!

::
/ ::

Warteschlange

klar