Phyzix - Again (Prod By Dare Devilz)

  • 4
  • 11
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0

Stream and download Phyzix - Phyzix - Again (Prod By Dare Devilz)

Letra

AGAIN by Phyzix
Produced by Dare Devilz
FIGARO 7 (2024)

INTRO
{Lighter, smoking and coughing sounds}

PRELUDE
Zachikondi ndazisiya
Zamalove ndazituluka
I will never ever ever fall in love again
I’ll ne hehehehe eh

VERSE 1
Akufuna kudumpha galimoto ikuyenda/ akuti chifukwa chikondi sichikuyenda/ chimakhala chani koma the other gender/ ku chipinda kwanga mawindo kumangogenda/ khungu langa so paliponse kumangosenda/ Instagram ndimupange unfollow Brenda/ ati simnzapeza mtendere back to sender/ ati afalitsa kuti sinditha kunye…/ chonsecho amakuwa mpaka kugwedeza denga/ akafuna kutukwana ndi ma middle finger/ komatu akufuna ndimuveke ring finger/// kugula magalasi amazangotenga/ zi ma monthly bundle daily amazapempha/ zi ma top zanga zonse anazitenga/ she’s a gaslighter ndi kamunthu kopenga koma kakamapita kumbuyo kuli uthenga

HOOK
Zachikondi ndazisiya
Zamalove ndazituluka
I will never ever ever fall in love again
I’ll never ever ever fall in love again x2

VERSE 2
Akuti ashowana ndi adani anga onse/ andiyalutsa azikamba nkhani zanga zonse/ zake zimenezo zindikhudze ndi Beyoncé?/ mesa nayenso ndi lokolo ngati ena tonse/ aliyense limankwanila lake la 40/ palibe wa pefekiti tonse ndi a ma fault/ za chikondi zimakhala bittersweet poetry/ ngati kumathamangitsa galimoto pali tree/ amafuna zi Ndalama pafupipafupi/ akavala ma skirt ndi afupiafupi/ amakonda zinthu kwambiri ngati ka groupie/ posting motivational quotes as if she push P/ amakonda ma hug nzingokhalira who's he?/ munthu wosapanga kalikonse koma busy/ mwina ndi wa business kapena wa beansness/ koma chomwe ndimadziwa amakonda chinyezi

HOOK
Zachikondi ndazisiya (uh yeah)
Zamalove ndazituluka (uh yeah)
I will never ever ever fall in love again (fall in love again)
I’ll never ever ever fall in love again (fall in love again) x4

OUTRO
Fall in love again
Fall in love again
Fall in love again
It’s Only Entertainment!

::
/ ::

Cola

Claro