Phyzix - Chimkazi (Prod By Mada The Drumkit & Pon G)

  • 17
  • 23
  • 1
  • 0
  • 0
  • 0
  • 0

Stream and download Phyzix - Chimkazi (Prod By Mada The Drumkit & Pon G)

Lirik

CHIMKAZI by Phyzix
Produced by Mada the Drumkit & Pon G
FIGARO 7 (2024)

INTRO
Mada on the track nigga
Anatenga chimkazi
I love it/ yeah
One two one two/ yeah
Yeah/ one two one two
Pon G on the board

PRELUDE
Nkhani ya chimkazi chomwe chinkafuna kuti tipange showbizz/ tibhebhetse pa Malawi tizipatse nthawi nkhani za chikondizi/ asee

VERSE 1
Ndinakumana ndi chimkazi ku epic/ macheza anayambira ndi zi ma pic/ amafuna kuti titenge ma selfie/ m'nali ndi thukuta nakapukuta Ku VIP/ anandiyamikira kuti Phyzo you push P/ uli ngati ine ndemwe you don't know what we could be/ we can be a power couple man just you and me/ tiwaphunzitse anthuwa how things should be/ za matchenedwe matchukidwe machitidwe / ndiwe dolo kale uli patali goat way/ tikaphatikizana tigwetsa onse/ nditenga deal ya premier bet iwe ya Betway/ mafana onsewa tiwakoleka mu khwekhwe/ ngati Rihanna ndi Drake nafenso ndi work work/ tinatengana ndikumapita panja/ nyimbo zanga m'galimoto playlist titasanja

HOOK
Nkhani ya chimkazi chomwe chinkafuna kuti tipange showbizz/ tibhebhetse pa Malawi tizipatse nthawi nkhani za chikondizi/ asee
Nkhani ya chimkazi chomwe chinkafuna kuti tipange showbizz/ tikometse pa Malawi ndinalibe machawi chinatengedwa chimkazi/ asee

VERSE 2
Tinapita President's hotel for coffee/ panalibe wamanyazi tonse ndi a confi/ tinakamba nkhani zambiri we both free/ amati akhala manager wanga at my girl's fee/ komanso akamayankhula amafusa ukundimva Phy?/ kundimvetsa kukoma kumudzutsa gadafi/ tinali limodzi for 5 hours roughly/ kucheza zinkhani kumangoseka laughing// anandiletsa kuvala ma t-shirt azidole/ ti ma show tondiphweketsa ndisamalole/ ndisanatuluke ndichedwe pa kalilole ndidzikankha zingini zanga mpaka dziko lilole/ tinatengerana kwa friend ku gulliver/ uku ndikomwe ndinalima munda kugalauza/ ndineyo kapena iyeyo anandiuser/ koma musadabwepo inu Andrew Matrauza

HOOK
Nkhani ya chimkazi chomwe chinkafuna kuti tipange showbizz/ tibhebhetse pa Malawi tizipatse nthawi nkhani za chikondizi/ asee
Nkhani ya chimkazi chomwe chinkafuna kuti tipange showbizz/ tikometse pa Malawi ndinalibe machawi chinatengedwa chimkazi/ asee

OUTRO
Anatenga Chimkazi
Chinapita Chimkazi
Anatenga Chimkazi
Chinapita Chimkazi

Hehehehehe ih guys
It’s Only Entertainment!

::
/ ::

Antre

Jernih